-
Oweruza 6:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Ndiyeno Gidiyoni anayankha kuti: “Pepani mbuyanga, koma ngati Yehova ali ndi ife, n’chifukwa chiyani zonsezi zatigwera?+ Nanga ntchito zake zodabwitsa zija,+ zimene makolo athu anatisimbira zili kuti?+ Iwo anatiuza kuti, ‘Yehova ndiye anatitulutsa mu Iguputo.’+ Koma tsopano Yehova watisiya,+ ndipo watipereka m’manja mwa Amidiyani.”
-