Yesaya 57:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 amene mumadzutsa chilakolako chanu pakati pa mitengo ikuluikulu+ ndi pansi pa mtengo uliwonse wa masamba ambiri?+ Kodi si inu amene mumapha ana m’zigwa* pakati pa matanthwe?+ Yeremiya 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Yehova anapitiriza kulankhula nane m’masiku a Mfumu Yosiya kuti:+ “‘Kodi waona zimene Isiraeli wosakhulupirikayu akuchita?+ Akupita kuphiri lililonse lalitali+ ndi pansi pa mtengo uliwonse waukulu wa masamba ambiri obiriwira+ kuti akachite uhule kumeneko.+ Yeremiya 17:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ngakhale ana awo aamuna akumbukira maguwa awo ansembe ndi mizati yawo yopatulika imene ili pansi pa mtengo waukulu wamasamba ambiri obiriwira, pamwamba pa zitunda zazitali+
5 amene mumadzutsa chilakolako chanu pakati pa mitengo ikuluikulu+ ndi pansi pa mtengo uliwonse wa masamba ambiri?+ Kodi si inu amene mumapha ana m’zigwa* pakati pa matanthwe?+
6 Yehova anapitiriza kulankhula nane m’masiku a Mfumu Yosiya kuti:+ “‘Kodi waona zimene Isiraeli wosakhulupirikayu akuchita?+ Akupita kuphiri lililonse lalitali+ ndi pansi pa mtengo uliwonse waukulu wa masamba ambiri obiriwira+ kuti akachite uhule kumeneko.+
2 Ngakhale ana awo aamuna akumbukira maguwa awo ansembe ndi mizati yawo yopatulika imene ili pansi pa mtengo waukulu wamasamba ambiri obiriwira, pamwamba pa zitunda zazitali+