-
Amosi 9:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Ndinaona Yehova ataima pamwamba pa guwa lansembe,+ ndipo anati: “Menya mutu wa chipilala kuti maziko ake agwedezeke ndipo udulenso mitu ya zipilala zonse.+ Ndiyeno otsala mwa anthuwo ndidzawapha ndi lupanga. Aliyense wa iwo amene adzathawa ndidzamuphabe, aliyense wa iwo amene adzathawa sadzapulumuka.+
-