Nehemiya 9:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “Koma iwo anakhala osamvera+ ndipo anakupandukirani.+ Anapitiriza kufulatira chilamulo chanu,+ ndipo anapha aneneri anu+ amene anali kuwalimbikitsa kuti abwerere kwa inu.+ Iwo anapitiriza kuchita zinthu zikuluzikulu zosakulemekezani.+ Yesaya 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Imvani+ kumwamba inu, ndipo tchera khutu iwe dziko lapansi, chifukwa Yehova wanena kuti: “Ndalera ana ndi kuwakulitsa,+ koma iwo andipandukira.+ Danieli 9:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ife tachimwa,+ talakwa, tachita zinthu zoipa ndipo takupandukirani.+ Tapatuka ndiponso tasiya malamulo anu ndi zigamulo zanu.+
26 “Koma iwo anakhala osamvera+ ndipo anakupandukirani.+ Anapitiriza kufulatira chilamulo chanu,+ ndipo anapha aneneri anu+ amene anali kuwalimbikitsa kuti abwerere kwa inu.+ Iwo anapitiriza kuchita zinthu zikuluzikulu zosakulemekezani.+
2 Imvani+ kumwamba inu, ndipo tchera khutu iwe dziko lapansi, chifukwa Yehova wanena kuti: “Ndalera ana ndi kuwakulitsa,+ koma iwo andipandukira.+
5 Ife tachimwa,+ talakwa, tachita zinthu zoipa ndipo takupandukirani.+ Tapatuka ndiponso tasiya malamulo anu ndi zigamulo zanu.+