Levitiko 13:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Ndiyeno zovala za munthu amene am’peza ndi khateyo zizing’ambidwa.+ Munthuyo asamakonze tsitsi lake+ ndipo aziphimba ndevu zake zapamlomo+ ndi kufuula kuti, ‘Wodetsedwa, wodetsedwa!’+
45 Ndiyeno zovala za munthu amene am’peza ndi khateyo zizing’ambidwa.+ Munthuyo asamakonze tsitsi lake+ ndipo aziphimba ndevu zake zapamlomo+ ndi kufuula kuti, ‘Wodetsedwa, wodetsedwa!’+