Yesaya 54:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Inetu ndi amene ndinalenga mmisiri, amene amauzira+ moto wamakala+ n’kupanga chida chankhondo ndi luso lake. Inenso ndi amene ndinalenga munthu wowononga,+ amene amagwira ntchito yowononga ena. Yeremiya 6:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Zipangizo zopemerera moto+ zatenthedwa ndi moto ndipo pamoto wawo pakutuluka mtovu.+ Munthu wakhala akuyenga chitsulo mobwerezabwereza koma osaphula kanthu, ndipo zoipa sizinachotsedwemo.+
16 “Inetu ndi amene ndinalenga mmisiri, amene amauzira+ moto wamakala+ n’kupanga chida chankhondo ndi luso lake. Inenso ndi amene ndinalenga munthu wowononga,+ amene amagwira ntchito yowononga ena.
29 Zipangizo zopemerera moto+ zatenthedwa ndi moto ndipo pamoto wawo pakutuluka mtovu.+ Munthu wakhala akuyenga chitsulo mobwerezabwereza koma osaphula kanthu, ndipo zoipa sizinachotsedwemo.+