Ezekieli 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Ine ndidzakumanga ndi zingwe+ kuti usatembenukire kumbali ina, mpaka utamaliza masiku ako ozungulira mzindawo. Yohane 21:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndithudi ndikukuuza iwe, Pamene unali mnyamata, unali kuvala wekha ndi kupita kumene unali kufuna. Koma ukadzakalamba, udzatambasula manja ako ndipo munthu wina adzakuveka,+ ndi kukunyamula kupita nawe kumene iwe sukufuna.”+ Machitidwe 20:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Chimodzi chokha chimene ndikudziwa n’chakuti mumzinda ndi mzinda, mzimu woyera+ wandichitira umboni mobwerezabwereza kuti maunyolo ndi masautso akundiyembekezera.+
8 “Ine ndidzakumanga ndi zingwe+ kuti usatembenukire kumbali ina, mpaka utamaliza masiku ako ozungulira mzindawo.
18 Ndithudi ndikukuuza iwe, Pamene unali mnyamata, unali kuvala wekha ndi kupita kumene unali kufuna. Koma ukadzakalamba, udzatambasula manja ako ndipo munthu wina adzakuveka,+ ndi kukunyamula kupita nawe kumene iwe sukufuna.”+
23 Chimodzi chokha chimene ndikudziwa n’chakuti mumzinda ndi mzinda, mzimu woyera+ wandichitira umboni mobwerezabwereza kuti maunyolo ndi masautso akundiyembekezera.+