Ezekieli 26:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndidzakusandutsa malo osalala apathanthwe lopanda kanthu.+ Udzakhala malo oyanikapo makoka.+ Iwe sudzamangidwanso, pakuti ine Yehova ndanena,’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.+
14 Ndidzakusandutsa malo osalala apathanthwe lopanda kanthu.+ Udzakhala malo oyanikapo makoka.+ Iwe sudzamangidwanso, pakuti ine Yehova ndanena,’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.+