Numeri 14:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 ‘Chifukwa Yehova analephera kufikitsa anthuwo kudziko limene anawalumbirira, anangowaphera m’chipululu.’+ Yoswa 7:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Akanani ndi anthu onse a m’dziko lino adzamva zimenezi, ndipo adzatizinga ndithu, ndi kufafaniza dzina lathu kulichotsa padziko lapansi.+ Nanga zikatero mudzaliteteza bwanji dzina lanu lalikulu?”+
16 ‘Chifukwa Yehova analephera kufikitsa anthuwo kudziko limene anawalumbirira, anangowaphera m’chipululu.’+
9 Akanani ndi anthu onse a m’dziko lino adzamva zimenezi, ndipo adzatizinga ndithu, ndi kufafaniza dzina lathu kulichotsa padziko lapansi.+ Nanga zikatero mudzaliteteza bwanji dzina lanu lalikulu?”+