Chivumbulutso 11:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mitundu ya anthu, mafuko, zinenero, ndi mayiko,+ adzayang’anitsitsa mitembo yawo masiku atatu ndi hafu,+ ndipo sadzalola kuti mitemboyo iikidwe m’manda.
9 Mitundu ya anthu, mafuko, zinenero, ndi mayiko,+ adzayang’anitsitsa mitembo yawo masiku atatu ndi hafu,+ ndipo sadzalola kuti mitemboyo iikidwe m’manda.