Numeri 16:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kodi amuna inu mukuyesa n’chinthu chaching’ono kuti Mulungu wa Isiraeli anakupatulani+ pakati pa Aisiraeli, n’kukutengani kukhala akeake, kuti muzitumikira Yehova pachihema chake ndi kutumikira khamulo?+
9 Kodi amuna inu mukuyesa n’chinthu chaching’ono kuti Mulungu wa Isiraeli anakupatulani+ pakati pa Aisiraeli, n’kukutengani kukhala akeake, kuti muzitumikira Yehova pachihema chake ndi kutumikira khamulo?+