Ekisodo 28:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 “Ana a Aroni uwapangire mikanjo+ ndi malamba ake. Uwapangirenso mipango*+ yokulunga kumutu kuti iwapatse ulemerero ndi kuwakongoletsa.+ Ekisodo 39:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndiyeno anapanga nduwira+ ya nsalu yabwino kwambiri, mipango yokongola yokulunga kumutu+ ya nsalu zabwino kwambiri ndi makabudula a nsalu+ za ulusi wopota wabwino kwambiri.
40 “Ana a Aroni uwapangire mikanjo+ ndi malamba ake. Uwapangirenso mipango*+ yokulunga kumutu kuti iwapatse ulemerero ndi kuwakongoletsa.+
28 Ndiyeno anapanga nduwira+ ya nsalu yabwino kwambiri, mipango yokongola yokulunga kumutu+ ya nsalu zabwino kwambiri ndi makabudula a nsalu+ za ulusi wopota wabwino kwambiri.