Ezekieli 21:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Iwe mwana wa munthu, losera ndipo uwombe m’manja.+ Unene katatu mawu akuti ‘Lupanga!’+ Limeneli ndi lupanga lopha anthu. Lupanga limeneli ndi limene lapha munthu wotchuka, ndipo lazungulira anthu.+
14 “Iwe mwana wa munthu, losera ndipo uwombe m’manja.+ Unene katatu mawu akuti ‘Lupanga!’+ Limeneli ndi lupanga lopha anthu. Lupanga limeneli ndi limene lapha munthu wotchuka, ndipo lazungulira anthu.+