2 Mafumu 21:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma sanamvere,+ ndipo Manase anapitiriza kunyengerera anthu kuti achite zinthu zoipa+ kuposa zimene inkachita mitundu+ yomwe Yehova anaiwononga pamaso pa ana a Isiraeli. Ezekieli 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye anapandukira zigamulo zanga pochita zoipa zoposa za mitundu ya anthuwo.+ Anapandukiranso malamulo anga kuposa mayiko amene amuzungulira, pakuti iye anakana zigamulo zanga ndipo sanayende m’malamulo anga.’+
9 Koma sanamvere,+ ndipo Manase anapitiriza kunyengerera anthu kuti achite zinthu zoipa+ kuposa zimene inkachita mitundu+ yomwe Yehova anaiwononga pamaso pa ana a Isiraeli.
6 Iye anapandukira zigamulo zanga pochita zoipa zoposa za mitundu ya anthuwo.+ Anapandukiranso malamulo anga kuposa mayiko amene amuzungulira, pakuti iye anakana zigamulo zanga ndipo sanayende m’malamulo anga.’+