-
Hoseya 4:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Iwo amapereka nsembe pamwamba pa mapiri+ ndipo amafukiza nsembe zautsi pazitunda.+ Amachitanso zimenezi pansi pa zimitengo zikuluzikulu, mitengo ya mlanje, ndi mitengo yaikulu, chifukwa ili ndi mthunzi wabwino.+ N’chifukwa chake ana anu aakazi amachita dama ndipo apongozi anu aakazi amachita chigololo.
-