Salimo 34:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Patukani pa zinthu zoipa ndipo chitani zabwino.+Funafunani mtendere ndi kuusunga.+ Yesaya 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Sambani,+ dziyeretseni.+ Chotsani zochita zanu zoipa pamaso panga.+ Lekani kuchita zoipa.+