Salimo 51:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Inu Mulungu, lengani mtima wolungama mkati mwanga,+Ndipo ikani maganizo* atsopano ndi okhazikika mwa ine.+ Yeremiya 32:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Ndidzawapatsa mtima umodzi+ ndi kuwachititsa kuyenda m’njira imodzi kuti azindiopa nthawi zonse. Ndidzatero kuti iwo pamodzi ndi ana awo zinthu ziwayendere bwino.+
10 Inu Mulungu, lengani mtima wolungama mkati mwanga,+Ndipo ikani maganizo* atsopano ndi okhazikika mwa ine.+
39 Ndidzawapatsa mtima umodzi+ ndi kuwachititsa kuyenda m’njira imodzi kuti azindiopa nthawi zonse. Ndidzatero kuti iwo pamodzi ndi ana awo zinthu ziwayendere bwino.+