Ekisodo 32:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Aiguputo+ anenerenji kuti, ‘Anawatulutsa m’dziko lino kuti akawaphe kumapiri ndi kuwafafaniza padziko lapansi’?+ Bwezani mkwiyo wanu woyaka motowo,+ ndipo mverani chisoni+ anthu anu kuti musawagwetsere tsoka. Numeri 14:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma Mose anamuyankha Yehova kuti: “Mukatero, Aiguputo amene munalanditsako anthuwa mwa mphamvu zanu, adzamva ndithu zimenezi.+ Deuteronomo 9:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 kuopera kuti anthu a m’dziko+ limene munatitulutsamo anganene kuti: “Chifukwa Yehova sanathe kuwalowetsa m’dziko limene anawalonjeza, komanso chifukwa chakuti anali kudana nawo, anawatulutsa kuti akawaphere m’chipululu.”+ Yoswa 7:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Akanani ndi anthu onse a m’dziko lino adzamva zimenezi, ndipo adzatizinga ndithu, ndi kufafaniza dzina lathu kulichotsa padziko lapansi.+ Nanga zikatero mudzaliteteza bwanji dzina lanu lalikulu?”+ 1 Samueli 12:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Chifukwa cha dzina lake lalikulu,+ Yehova sadzasiya+ anthu ake, pakuti Yehova wafuna kuti inuyo mukhale anthu ake.+
12 Aiguputo+ anenerenji kuti, ‘Anawatulutsa m’dziko lino kuti akawaphe kumapiri ndi kuwafafaniza padziko lapansi’?+ Bwezani mkwiyo wanu woyaka motowo,+ ndipo mverani chisoni+ anthu anu kuti musawagwetsere tsoka.
13 Koma Mose anamuyankha Yehova kuti: “Mukatero, Aiguputo amene munalanditsako anthuwa mwa mphamvu zanu, adzamva ndithu zimenezi.+
28 kuopera kuti anthu a m’dziko+ limene munatitulutsamo anganene kuti: “Chifukwa Yehova sanathe kuwalowetsa m’dziko limene anawalonjeza, komanso chifukwa chakuti anali kudana nawo, anawatulutsa kuti akawaphere m’chipululu.”+
9 Akanani ndi anthu onse a m’dziko lino adzamva zimenezi, ndipo adzatizinga ndithu, ndi kufafaniza dzina lathu kulichotsa padziko lapansi.+ Nanga zikatero mudzaliteteza bwanji dzina lanu lalikulu?”+
22 Chifukwa cha dzina lake lalikulu,+ Yehova sadzasiya+ anthu ake, pakuti Yehova wafuna kuti inuyo mukhale anthu ake.+