Salimo 115:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma Mulungu wathu ali kumwamba.+Chilichonse chimene anafuna kuchita anachita.+ Salimo 115:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kunena za kumwamba, kumwamba ndi kwa Yehova,+Koma dziko lapansi analipereka kwa ana a anthu.+