Salimo 36:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti inu ndinu kasupe wa moyo.+Chifukwa cha kuwala kochokera kwa inu, tikuona kuwala.+ Salimo 112:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Waunika mu mdima kuti anthu owongoka mtima aone kuwala.+ ח [Chehth]Iye ndi wachisomo, wachifundo ndi wolungama.+ 1 Yohane 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Umenewu ndi uthenga umene taumva kuchokera kwa iye ndipo tikuulengeza kwa inu,+ kuti Mulungu ndiye kuwala+ ndipo mwa iye mulibe mdima ngakhale pang’ono.+
4 Waunika mu mdima kuti anthu owongoka mtima aone kuwala.+ ח [Chehth]Iye ndi wachisomo, wachifundo ndi wolungama.+
5 Umenewu ndi uthenga umene taumva kuchokera kwa iye ndipo tikuulengeza kwa inu,+ kuti Mulungu ndiye kuwala+ ndipo mwa iye mulibe mdima ngakhale pang’ono.+