Salimo 97:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kuwala kwaunikira wolungama,+Ndipo anthu owongoka mtima akusangalala.+ Yesaya 11:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Sizidzavulazana+ kapena kuwonongana m’phiri langa lonse loyera,+ chifukwa dziko lapansi lidzadzaza ndi anthu odziwa Yehova ngati mmene madzi amadzazira nyanja.+ Yesaya 58:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 mukapatsa munthu wanjala zinthu zimene inuyo mumakonda,+ ndiponso mukakhutiritsa munthu amene akusautsidwa, kuunika kwanu kudzawala kuti ngwee! mu mdima, ndipo mdima wanu udzakhala ngati masana dzuwa likakhala paliwombo.+ Chivumbulutso 22:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mzimu+ ndi mkwatibwi+ akunenabe kuti: “Bwera!” Aliyense wakumva anene kuti: “Bwera!”+ Aliyense wakumva ludzu abwere.+ Aliyense amene akufuna, amwe madzi a moyo kwaulere.+
9 Sizidzavulazana+ kapena kuwonongana m’phiri langa lonse loyera,+ chifukwa dziko lapansi lidzadzaza ndi anthu odziwa Yehova ngati mmene madzi amadzazira nyanja.+
10 mukapatsa munthu wanjala zinthu zimene inuyo mumakonda,+ ndiponso mukakhutiritsa munthu amene akusautsidwa, kuunika kwanu kudzawala kuti ngwee! mu mdima, ndipo mdima wanu udzakhala ngati masana dzuwa likakhala paliwombo.+
17 Mzimu+ ndi mkwatibwi+ akunenabe kuti: “Bwera!” Aliyense wakumva anene kuti: “Bwera!”+ Aliyense wakumva ludzu abwere.+ Aliyense amene akufuna, amwe madzi a moyo kwaulere.+