2 Mafumu 10:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Koma Yehu sanayesetse kuyenda motsatira malamulo a Yehova Mulungu wa Isiraeli ndi mtima wake wonse.+ Sanapatuke pa machimo a Yerobowamu amene anachimwitsa nawo Isiraeli.+
31 Koma Yehu sanayesetse kuyenda motsatira malamulo a Yehova Mulungu wa Isiraeli ndi mtima wake wonse.+ Sanapatuke pa machimo a Yerobowamu amene anachimwitsa nawo Isiraeli.+