Yesaya 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Masomphenya+ amene Yesaya+ mwana wa Amozi anaona, okhudza Yuda ndi Yerusalemu m’masiku a Uziya,+ Yotamu,+ Ahazi+ ndi Hezekiya,+ mafumu a Yuda:+ Mika 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 M’masiku a Yotamu,+ Ahazi+ ndi Hezekiya,+ mafumu a Yuda,+ Yehova analankhula ndi Mika+ wa ku Moreseti kudzera m’masomphenya. M’masomphenyawo anamuuza zokhudza Samariya+ ndi Yerusalemu+ kuti:
1 Masomphenya+ amene Yesaya+ mwana wa Amozi anaona, okhudza Yuda ndi Yerusalemu m’masiku a Uziya,+ Yotamu,+ Ahazi+ ndi Hezekiya,+ mafumu a Yuda:+
1 M’masiku a Yotamu,+ Ahazi+ ndi Hezekiya,+ mafumu a Yuda,+ Yehova analankhula ndi Mika+ wa ku Moreseti kudzera m’masomphenya. M’masomphenyawo anamuuza zokhudza Samariya+ ndi Yerusalemu+ kuti: