Yesaya 59:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ife taphwanya malamulo ndipo tamukana Yehova.+ Tabwerera m’mbuyo n’kumusiya Mulungu wathu. Tanena zinthu zopondereza ena ndi zopanduka.+ Taganiza mawu achinyengo mumtima mwathu n’kumawalankhula chapansipansi.+
13 Ife taphwanya malamulo ndipo tamukana Yehova.+ Tabwerera m’mbuyo n’kumusiya Mulungu wathu. Tanena zinthu zopondereza ena ndi zopanduka.+ Taganiza mawu achinyengo mumtima mwathu n’kumawalankhula chapansipansi.+