Yeremiya 12:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Afesa tirigu koma akolola minga.+ Agwira ntchito mpaka kudwala nayo, koma osapeza phindu lililonse.+ Iwo adzachita manyazi ndi zokolola zawo chifukwa mkwiyo waukulu wa Yehova udzawayakira.”
13 Afesa tirigu koma akolola minga.+ Agwira ntchito mpaka kudwala nayo, koma osapeza phindu lililonse.+ Iwo adzachita manyazi ndi zokolola zawo chifukwa mkwiyo waukulu wa Yehova udzawayakira.”