Yesaya 8:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Inu mitundu ya anthu, vulazani anthu, koma inuyo muphwanyidwaphwanyidwa. Inu nonse amene muli kumalekezero a dziko lapansi, tamverani.+ Nyamulani zida zankhondo+ koma muphwanyidwaphwanyidwa.+ Nyamulani zida zankhondo koma muphwanyidwaphwanyidwa. Yeremiya 46:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Amuna inu, tengani zishango zanu zazikulu ndi zazing’ono ndipo konzekerani kumenya nkhondo.+
9 Inu mitundu ya anthu, vulazani anthu, koma inuyo muphwanyidwaphwanyidwa. Inu nonse amene muli kumalekezero a dziko lapansi, tamverani.+ Nyamulani zida zankhondo+ koma muphwanyidwaphwanyidwa.+ Nyamulani zida zankhondo koma muphwanyidwaphwanyidwa.