Genesis 37:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Pamenepo Yakobo anang’amba zovala zake, n’kuvala chiguduli* m’chiuno mwake, ndipo anamulira mwana wake masiku ambiri.+ 2 Samueli 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Davide atamva zimenezi anagwira zovala zake ndi kuzing’amba.+ Nawonso amuna onse amene anali ndi Davide anang’amba zovala zawo.
34 Pamenepo Yakobo anang’amba zovala zake, n’kuvala chiguduli* m’chiuno mwake, ndipo anamulira mwana wake masiku ambiri.+
11 Davide atamva zimenezi anagwira zovala zake ndi kuzing’amba.+ Nawonso amuna onse amene anali ndi Davide anang’amba zovala zawo.