Yeremiya 9:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Yehova wa makamu wanena kuti, ‘Chitani zinthu mozindikira anthu inu, ndipo itanani akazi oimba nyimbo zoimba polira kuti abwere.+ Tumizani anthu kuti akaitane akazi odziwa kulira maliro,+
17 “Yehova wa makamu wanena kuti, ‘Chitani zinthu mozindikira anthu inu, ndipo itanani akazi oimba nyimbo zoimba polira kuti abwere.+ Tumizani anthu kuti akaitane akazi odziwa kulira maliro,+