Maliro 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yehova wakhala ngati mdani.+ Wameza Isiraeli.+Iye wameza nsanja zonse za Isiraeli zokhalamo.+ Wawononga malo ake otetezedwa ndiponso mipanda yolimba kwambiri.+Wachititsa kuti kulira ndi maliro+ zimveke mumzinda wa mwana wamkazi wa Yuda.
5 Yehova wakhala ngati mdani.+ Wameza Isiraeli.+Iye wameza nsanja zonse za Isiraeli zokhalamo.+ Wawononga malo ake otetezedwa ndiponso mipanda yolimba kwambiri.+Wachititsa kuti kulira ndi maliro+ zimveke mumzinda wa mwana wamkazi wa Yuda.