Amosi 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Tsopano zinthu zofanana ndi zimenezi ndi zimene ndidzakuchitira, iwe Isiraeli. Ndipo chifukwa chakuti ndidzakuchitira zimenezi, konzekera kukumana ndi Mulungu wako,+ iwe Isiraeli. Amosi 7:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno Yehova anandifunsa kuti: “Kodi ukuona chiyani Amosi?” Ndinamuyankha kuti: “Ndikuona chingwe chowongolera.” Pamenepo Yehova anati: “Ine ndiika chingwe chowongolera pakati pa anthu anga Aisiraeli,+ ndipo sindidzawakhululukiranso.+
12 “Tsopano zinthu zofanana ndi zimenezi ndi zimene ndidzakuchitira, iwe Isiraeli. Ndipo chifukwa chakuti ndidzakuchitira zimenezi, konzekera kukumana ndi Mulungu wako,+ iwe Isiraeli.
8 Ndiyeno Yehova anandifunsa kuti: “Kodi ukuona chiyani Amosi?” Ndinamuyankha kuti: “Ndikuona chingwe chowongolera.” Pamenepo Yehova anati: “Ine ndiika chingwe chowongolera pakati pa anthu anga Aisiraeli,+ ndipo sindidzawakhululukiranso.+