Yeremiya 15:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mkazi amene wabereka ana 7 wafooka ndipo akupuma movutikira.+ Kwa iye dzuwa lalowa masanasana,+ ndipo lachita manyazi ndi kuthedwa nzeru. Anthu otsala ndidzawapereka kwa adani awo kuti aphedwe ndi lupanga,’+ watero Yehova.” Mika 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 ‘Choncho anthu inu usiku udzakufikirani,+ ndipo simudzaonanso masomphenya.+ Mudzangoona mdima wokhawokha moti simudzaloseranso. Aneneri amenewa dzuwa lidzawalowera ndipo mdima udzawagwera masanasana.+ Mateyu 24:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 “Chisautso cha masiku amenewo chikadzangotha, dzuwa lidzachita mdima+ ndipo mwezi+ sudzapereka kuwala kwake. Nyenyezi zidzagwa kuchokera kumwamba, ndipo mphamvu za kumwamba zidzagwedezeka.+
9 Mkazi amene wabereka ana 7 wafooka ndipo akupuma movutikira.+ Kwa iye dzuwa lalowa masanasana,+ ndipo lachita manyazi ndi kuthedwa nzeru. Anthu otsala ndidzawapereka kwa adani awo kuti aphedwe ndi lupanga,’+ watero Yehova.”
6 ‘Choncho anthu inu usiku udzakufikirani,+ ndipo simudzaonanso masomphenya.+ Mudzangoona mdima wokhawokha moti simudzaloseranso. Aneneri amenewa dzuwa lidzawalowera ndipo mdima udzawagwera masanasana.+
29 “Chisautso cha masiku amenewo chikadzangotha, dzuwa lidzachita mdima+ ndipo mwezi+ sudzapereka kuwala kwake. Nyenyezi zidzagwa kuchokera kumwamba, ndipo mphamvu za kumwamba zidzagwedezeka.+