Zefaniya 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pa tsiku limenelo, ndidzalanga aliyense amene ali pafupi ndi mpando wachifumu, anthu amene adzaza nyumba za ambuye awo ndi chiwawa ndiponso chinyengo.+
9 Pa tsiku limenelo, ndidzalanga aliyense amene ali pafupi ndi mpando wachifumu, anthu amene adzaza nyumba za ambuye awo ndi chiwawa ndiponso chinyengo.+