Amosi 6:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Anthu inu mukugona pamipando ya minyanga ya njovu+ ndi kudziwongola pamabedi, ndiponso mukudya nyama ya ana a nkhosa ndi ana amphongo onenepa a ng’ombe zanu.+
4 Anthu inu mukugona pamipando ya minyanga ya njovu+ ndi kudziwongola pamabedi, ndiponso mukudya nyama ya ana a nkhosa ndi ana amphongo onenepa a ng’ombe zanu.+