Ekisodo 32:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Tsopano atsogolere anthuwa kumalo amene ndakuuza. Taona! Mngelo wanga akhala patsogolo panu,+ ndipo pa tsiku langa lopereka chilango, ndidzawalangadi chifukwa cha tchimo lawo.”+ Yeremiya 9:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Yehova wanena kuti, “Taona masiku akubwera ndipo ndidzaimba mlandu aliyense wodulidwa koma amene sanachite mdulidwe wa mtima wake.+ Hoseya 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Zimene zidzachitikira anthuwo zidzachitikiranso ansembe.+ Ndidzawaimba mlandu onsewa chifukwa cha njira zawo+ ndipo ndidzawabwezera zochita zawo.+
34 Tsopano atsogolere anthuwa kumalo amene ndakuuza. Taona! Mngelo wanga akhala patsogolo panu,+ ndipo pa tsiku langa lopereka chilango, ndidzawalangadi chifukwa cha tchimo lawo.”+
25 Yehova wanena kuti, “Taona masiku akubwera ndipo ndidzaimba mlandu aliyense wodulidwa koma amene sanachite mdulidwe wa mtima wake.+
9 “Zimene zidzachitikira anthuwo zidzachitikiranso ansembe.+ Ndidzawaimba mlandu onsewa chifukwa cha njira zawo+ ndipo ndidzawabwezera zochita zawo.+