Deuteronomo 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Tsopano amenewa ndiwo malamulo, malangizo ndi zigamulo zimene Yehova Mulungu wanu walamula kuti ndikuphunzitseni,+ kuti muzikazitsatira m’dziko limene mukuwolokerako kukalitenga kukhala lanu. Salimo 25:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Adzachititsa ofatsa kutsatira zigamulo zake,+Ndipo adzaphunzitsa ofatsa kuyenda m’njira yake.+ Yohane 6:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Zinalembedwa m’Mabuku a Aneneri kuti, ‘Ndipo onse adzaphunzitsidwa ndi Yehova.’*+ Aliyense amene wamva kwa Atate ndipo waphunzira amabwera kwa ine.+
6 “Tsopano amenewa ndiwo malamulo, malangizo ndi zigamulo zimene Yehova Mulungu wanu walamula kuti ndikuphunzitseni,+ kuti muzikazitsatira m’dziko limene mukuwolokerako kukalitenga kukhala lanu.
45 Zinalembedwa m’Mabuku a Aneneri kuti, ‘Ndipo onse adzaphunzitsidwa ndi Yehova.’*+ Aliyense amene wamva kwa Atate ndipo waphunzira amabwera kwa ine.+