Yesaya 54:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iwe udzakhazikika m’chilungamo.+ Kuponderezedwa udzatalikirana nako,+ ndipo sudzaopa aliyense. Chilichonse choopsa udzatalikirana nacho, pakuti sichidzakuyandikira.+ Ezekieli 34:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 “‘“Ine ndidzachita nazo pangano la mtendere.+ Ndidzachotsa zilombo zolusa zakutchire m’dzikomo.+ Nkhosazo zidzakhala m’chipululu popanda choziopsa ndipo zizidzagona m’nkhalango.+ Ezekieli 39:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Akadzakhala m’dziko lawo mwabata+ popanda wowaopsa,+ adzakhala atachita manyazi mokwanira+ chifukwa cha zinthu zonse zosakhulupirika zimene anandichitira.+
14 Iwe udzakhazikika m’chilungamo.+ Kuponderezedwa udzatalikirana nako,+ ndipo sudzaopa aliyense. Chilichonse choopsa udzatalikirana nacho, pakuti sichidzakuyandikira.+
25 “‘“Ine ndidzachita nazo pangano la mtendere.+ Ndidzachotsa zilombo zolusa zakutchire m’dzikomo.+ Nkhosazo zidzakhala m’chipululu popanda choziopsa ndipo zizidzagona m’nkhalango.+
26 Akadzakhala m’dziko lawo mwabata+ popanda wowaopsa,+ adzakhala atachita manyazi mokwanira+ chifukwa cha zinthu zonse zosakhulupirika zimene anandichitira.+