1 Samueli 24:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Yehova akhale woweruza, ndipo aweruze pakati pa ine ndi inu. Iye adzandiweruzira mlanduwu+ ndi kuchitapo kanthu kuti andimasule m’manja mwanu.” Chivumbulutso 18:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “Kondwerani kumwambako+ chifukwa cha zimene zamuchitikira. Inunso oyera,+ inu atumwi,+ ndi inu aneneri, kondwerani chifukwa Mulungu wamuweruza ndi kumupatsa chilango chifukwa cha zomwe anakuchitirani.”+
15 Yehova akhale woweruza, ndipo aweruze pakati pa ine ndi inu. Iye adzandiweruzira mlanduwu+ ndi kuchitapo kanthu kuti andimasule m’manja mwanu.”
20 “Kondwerani kumwambako+ chifukwa cha zimene zamuchitikira. Inunso oyera,+ inu atumwi,+ ndi inu aneneri, kondwerani chifukwa Mulungu wamuweruza ndi kumupatsa chilango chifukwa cha zomwe anakuchitirani.”+