Yobu 9:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iye ali ndi mtima wanzeru ndiponso mphamvu zambiri.+Ndani angachite naye makani,* koma osavulala?+ Salimo 62:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kawiri konse ndamva kuti Mulungu wanena kuti,+Mphamvu ndi za Mulungu.+ Aefeso 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 ndi kukula kwa mphamvu zake zopambana+ zimene wazipereka kwa ife okhulupirira. Kukula kumeneko n’kogwirizana ndi ntchito+ ya mphamvu yake yodabwitsa,
19 ndi kukula kwa mphamvu zake zopambana+ zimene wazipereka kwa ife okhulupirira. Kukula kumeneko n’kogwirizana ndi ntchito+ ya mphamvu yake yodabwitsa,