-
Ezara 6:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Tsopano akulu+ a Ayuda anali kupita patsogolo pa ntchito yomanga+ nyumbayo atalimbikitsidwa ndi ulosi wa mneneri Hagai+ ndi Zekariya+ mdzukulu wa Ido.+ Iwo anamanga nyumbayo ndi kuimaliza potsatira lamulo la Mulungu wa Isiraeli,+ ndi lamulo la Koresi,+ Dariyo,+ ndi Aritasasita+ mfumu ya Perisiya.
-