Yesaya 22:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “M’tsiku limenelo, Yehova wa makamu, Ambuye Wamkulu Koposa,+ adzalamula anthu kuti alire,+ agwetse misozi, amete mipala ndiponso avale ziguduli m’chiuno.+ Zekariya 7:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Kauze anthu onse a m’dzikoli ndi ansembe kuti, ‘Pamene munali kusala kudya+ ndi kulira m’mwezi wachisanu komanso m’mwezi wa 7+ kwa zaka 70,+ kodi munalidi kusala kudya chifukwa cha ine?+
12 “M’tsiku limenelo, Yehova wa makamu, Ambuye Wamkulu Koposa,+ adzalamula anthu kuti alire,+ agwetse misozi, amete mipala ndiponso avale ziguduli m’chiuno.+
5 “Kauze anthu onse a m’dzikoli ndi ansembe kuti, ‘Pamene munali kusala kudya+ ndi kulira m’mwezi wachisanu komanso m’mwezi wa 7+ kwa zaka 70,+ kodi munalidi kusala kudya chifukwa cha ine?+