Salimo 72:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Aweruze osautsika pakati pa anthu,+Apulumutse ana a anthu osauka,Ndipo aphwanye wobera anzake mwachinyengo. Miyambo 22:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Usabere munthu wonyozeka chifukwa chakuti ndi wonyozeka,+ ndipo usapondereze wosautsika pachipata cha mzinda.+
4 Aweruze osautsika pakati pa anthu,+Apulumutse ana a anthu osauka,Ndipo aphwanye wobera anzake mwachinyengo.
22 Usabere munthu wonyozeka chifukwa chakuti ndi wonyozeka,+ ndipo usapondereze wosautsika pachipata cha mzinda.+