Salimo 36:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ali pabedi lake amakonza chiwembu kuti apweteke anzake.+Amaima panjira yoipa.+Sapewa kuchita zinthu zoipa.+ Miyambo 6:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 mtima wokonzera ena ziwembu,+ mapazi othamangira kukachita zoipa,+ Zekariya 8:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Musamakonzerane ziwembu mumtima mwanu kuti muonetsane tsoka+ ndipo musamakonde kulumbira monama.+ Pakuti zinthu zonsezi ine ndimadana nazo,’+ watero Yehova.” Maliko 7:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pakuti mkatimo, mumtima mwa munthu,+ mumatuluka maganizo oipa. Mumatuluka zadama,*+ zakuba, zaumbanda,+
4 Ali pabedi lake amakonza chiwembu kuti apweteke anzake.+Amaima panjira yoipa.+Sapewa kuchita zinthu zoipa.+
17 Musamakonzerane ziwembu mumtima mwanu kuti muonetsane tsoka+ ndipo musamakonde kulumbira monama.+ Pakuti zinthu zonsezi ine ndimadana nazo,’+ watero Yehova.”
21 Pakuti mkatimo, mumtima mwa munthu,+ mumatuluka maganizo oipa. Mumatuluka zadama,*+ zakuba, zaumbanda,+