Yesaya 44:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Iwo sadziwa chilichonse+ ndipo samvetsetsa chilichonse+ chifukwa maso awo amatidwa kuti asamaone,+ ndipo mitima yawo ndi yosazindikira zinthu.+ Mateyu 13:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pakuti anthu awa aumitsa mtima wawo, ndipo amva ndi makutu awo koma osalabadira. Atseka maso awo kuti asaone ndi maso awo ndi kumva ndi makutu awo ndi kuzindikira tanthauzo lake m’mitima yawo n’kutembenuka, kuti ine ndiwachiritse.’+
18 Iwo sadziwa chilichonse+ ndipo samvetsetsa chilichonse+ chifukwa maso awo amatidwa kuti asamaone,+ ndipo mitima yawo ndi yosazindikira zinthu.+
15 Pakuti anthu awa aumitsa mtima wawo, ndipo amva ndi makutu awo koma osalabadira. Atseka maso awo kuti asaone ndi maso awo ndi kumva ndi makutu awo ndi kuzindikira tanthauzo lake m’mitima yawo n’kutembenuka, kuti ine ndiwachiritse.’+