1 Mafumu 1:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Mfumuyo inawauza kuti: “Tengani atumiki+ a mbuye wanu, n’kukweza Solomo mwana wanga panyulu* yanga yaikazi,+ ndipo mupite naye ku Gihoni.+ Mateyu 21:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iwo anabweretsa bulu uja limodzi ndi mwana wake wamphongo. Kenako anayala malaya awo akunja pa abuluwo ndipo iye anakwerapo.+
33 Mfumuyo inawauza kuti: “Tengani atumiki+ a mbuye wanu, n’kukweza Solomo mwana wanga panyulu* yanga yaikazi,+ ndipo mupite naye ku Gihoni.+
7 Iwo anabweretsa bulu uja limodzi ndi mwana wake wamphongo. Kenako anayala malaya awo akunja pa abuluwo ndipo iye anakwerapo.+