2 Samueli 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ngakhale zinali choncho, Davide analanda Ziyoni, malo okhala mumpanda wolimba kwambiri,+ umene ndi Mzinda wa Davide.+ Yeremiya 31:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pakuti tsiku lidzafika, pamene alonda amene ali m’mapiri a Efuraimu adzafuula kuti, ‘Nyamukani amuna inu, tiyeni tipite ku Ziyoni, kwa Yehova Mulungu wathu.’”+
7 Ngakhale zinali choncho, Davide analanda Ziyoni, malo okhala mumpanda wolimba kwambiri,+ umene ndi Mzinda wa Davide.+
6 Pakuti tsiku lidzafika, pamene alonda amene ali m’mapiri a Efuraimu adzafuula kuti, ‘Nyamukani amuna inu, tiyeni tipite ku Ziyoni, kwa Yehova Mulungu wathu.’”+