Mateyu 26:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 n’kuwafunsa kuti: “Kodi mudzandipatsa chiyani ndikamupereka kwa inu?”+ Iwo anamulonjeza ndalama 30 zasiliva.+ Mateyu 27:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pamenepo zimene zinanenedwa kudzera mwa mneneri Yeremiya* zinakwaniritsidwa. Iye anati: “Ndipo anatenga ndalama 30 zasiliva,+ zomwe zinali mtengo wogulira munthu umene ena mwa ana a Isiraeli anamuikira,
15 n’kuwafunsa kuti: “Kodi mudzandipatsa chiyani ndikamupereka kwa inu?”+ Iwo anamulonjeza ndalama 30 zasiliva.+
9 Pamenepo zimene zinanenedwa kudzera mwa mneneri Yeremiya* zinakwaniritsidwa. Iye anati: “Ndipo anatenga ndalama 30 zasiliva,+ zomwe zinali mtengo wogulira munthu umene ena mwa ana a Isiraeli anamuikira,