Yoweli 2:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ndiyeno aliyense woitana pa dzina la Yehova adzapulumuka,+ pakuti m’phiri la Ziyoni ndiponso mu Yerusalemu mudzakhala anthu opulumuka+ monga mmene Yehova ananenera. Amenewa ndi anthu amene Yehova akuwaitana.”+ Mateyu 24:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kunena zoona, masikuwo akanapanda kufupikitsidwa, palibe amene akanapulumuka. Koma chifukwa cha osankhidwawo,+ masikuwo adzafupikitsidwa.+ Aroma 9:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Komanso, Yesaya analankhula mofuula zokhudza Isiraeli kuti: “Ngakhale kuti ana a Isiraeli adzakhala ochuluka ngati mchenga wa m’nyanja,+ ndi ochepa okha amene adzapulumuke.+
32 Ndiyeno aliyense woitana pa dzina la Yehova adzapulumuka,+ pakuti m’phiri la Ziyoni ndiponso mu Yerusalemu mudzakhala anthu opulumuka+ monga mmene Yehova ananenera. Amenewa ndi anthu amene Yehova akuwaitana.”+
22 Kunena zoona, masikuwo akanapanda kufupikitsidwa, palibe amene akanapulumuka. Koma chifukwa cha osankhidwawo,+ masikuwo adzafupikitsidwa.+
27 Komanso, Yesaya analankhula mofuula zokhudza Isiraeli kuti: “Ngakhale kuti ana a Isiraeli adzakhala ochuluka ngati mchenga wa m’nyanja,+ ndi ochepa okha amene adzapulumuke.+