Zekariya 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Choncho Yehova wanena kuti, ‘“Ndithu ndidzabwerera ku Yerusalemu ndi kuchitira chifundo mzinda umenewu.+ Nyumba yanga idzamangidwa mmenemo,+ ndipo chingwe choyezera chidzatambasulidwa pa Yerusalemu,”+ watero Yehova wa makamu.’ Chivumbulutso 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiyeno ndinapatsidwa bango lokhala ngati ndodo+ ndipo ndinauzidwa kuti: “Nyamuka, kayeze nyumba yopatulika ya pakachisi+ wa Mulungu, guwa lansembe, ndi amene akulambira mmenemo.
16 “Choncho Yehova wanena kuti, ‘“Ndithu ndidzabwerera ku Yerusalemu ndi kuchitira chifundo mzinda umenewu.+ Nyumba yanga idzamangidwa mmenemo,+ ndipo chingwe choyezera chidzatambasulidwa pa Yerusalemu,”+ watero Yehova wa makamu.’
11 Ndiyeno ndinapatsidwa bango lokhala ngati ndodo+ ndipo ndinauzidwa kuti: “Nyamuka, kayeze nyumba yopatulika ya pakachisi+ wa Mulungu, guwa lansembe, ndi amene akulambira mmenemo.