Mateyu 13:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Zilekeni zonse zikulire pamodzi mpaka nthawi yokolola. M’nyengo yokolola ndidzauza okololawo kuti, Choyamba sonkhanitsani namsongole ndi kumumanga m’mitolo kuti akatenthedwe.+ Mukatha mupite kukasonkhanitsa tirigu ndi kumuika m’nkhokwe yanga.’”+
30 Zilekeni zonse zikulire pamodzi mpaka nthawi yokolola. M’nyengo yokolola ndidzauza okololawo kuti, Choyamba sonkhanitsani namsongole ndi kumumanga m’mitolo kuti akatenthedwe.+ Mukatha mupite kukasonkhanitsa tirigu ndi kumuika m’nkhokwe yanga.’”+