Deuteronomo 29:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 munaona zinthu zawo zonyansa ndi mafano awo onyansa,*+ mafano amtengo ndi amwala, asiliva ndi agolide amene anali nawo.) 1 Mafumu 11:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Solomo anayamba kutsatira Asitoreti,+ mulungu wamkazi wa Asidoni, ndi Milikomu,+ chonyansa cha Aamoni. Chivumbulutso 13:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndipo chinaloledwa kupereka mpweya ku chifaniziro cha chilombo chija, kuti chifaniziro cha chilombocho chithe kulankhula, ndi kuchititsa kuti onse amene mwa njira iliyonse salambira chifaniziro+ cha chilombocho, aphedwe.
17 munaona zinthu zawo zonyansa ndi mafano awo onyansa,*+ mafano amtengo ndi amwala, asiliva ndi agolide amene anali nawo.)
5 Solomo anayamba kutsatira Asitoreti,+ mulungu wamkazi wa Asidoni, ndi Milikomu,+ chonyansa cha Aamoni.
15 Ndipo chinaloledwa kupereka mpweya ku chifaniziro cha chilombo chija, kuti chifaniziro cha chilombocho chithe kulankhula, ndi kuchititsa kuti onse amene mwa njira iliyonse salambira chifaniziro+ cha chilombocho, aphedwe.